| This article must adhere to the biographies of living persons (BLP) policy, even if it is not a biography, because it contains material about living persons. Contentious material about living persons that is unsourced or poorly sourced must be removed immediately from the article and its talk page, especially if potentially libellous. If such material is repeatedly inserted, or if you have other concerns, please report the issue to this noticeboard.If you are a subject of this article, or acting on behalf of one, and you need help, please see this help page. |
| This article is rated Start-class on Wikipedia's content assessment scale. It is of interest to the following WikiProjects: | ||||||||||||||||||||||||||||||||||
| ||||||||||||||||||||||||||||||||||
Honorable
editZipangizo za ulimi zotsika mtengo. Boma linatiganizila ife a Malawi osaukitsitsa kuti tithe kufikila kugula zipangozozi kuno kwathu kwa Chimpumbulu T/A Chitukula, Lilongwe koma zomwe zikuchitika ndi dzinyengo anthu omwe mwawatuma kuti adzatigulitse zipangizozi kuti munthu agule ayeneleka kupelekanso ndalama ya lunch kuwonjezela apo omwe akugula zipangizozi ndi mavenda okha okha ife anthu akumudzi tikupempha kuti mutibweletsele achitetezo.Mwina anthu omwe mwawatuma wa ndi a opposition iyi a kupangayi ndi dikampeni yoti a Malawi ade kukhosi ndi Boma lomwe likulamulilali.Chonde bwana tithandizeni 137.196.0.28 (talk) 03:18, 13 November 2024 (UTC)

